Masalimo 41:4 - Buku Lopatulika4 Ndinati ine, Mundichitire chifundo, Yehova; Chiritsani mtima wanga; pakuti ndachimwira Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndinati ine, Mundichitire chifundo, Yehova; Chiritsani mtima wanga; pakuti ndachimwira Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono ndidati, “Inu Chauta, ndakuchimwirani, mundikomere mtima, muchiritse moyo wanga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndinati, “Inu Yehova, mundichitire chifundo; chiritseni pakuti ndakuchimwirani.” Onani mutuwo |