Masalimo 41:8 - Buku Lopatulika8 Chamgwera chinthu choopsa, ati; popeza ali gonire sadzaukanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chamgwera chinthu choopsa, ati; popeza ali gonire sadzaukanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Amati, “Yamgwera nthenda yofa nayo, sadzukanso pamene wagonapo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Matenda owopsa amugwira; sadzaukapo pamalo pamene wagona.” Onani mutuwo |