Weramutsani mitu yanu, zipata inu; inde weramutsani, zitseko zosatha inu, kuti Mfumu ya ulemerero ilowe.
Kankhani zipata za mzinda, tsekulani zitseko zakalekalezo, kuti Mfumu yaulemerero iloŵe.
Tukulani mitu yanu, inu zipata; tsekukani, inu zitseko zakalekalenu, kuti Mfumu yaulemerero ilowe.
Chipata cha Yehova ndi ichi; olungama adzalowamo.