Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Masalimo 148:9 - Buku Lopatulika

mapiri ndi zitunda zonse; mitengo yazipatso ndi yamikungudza yonse:

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

mapiri ndi zitunda zonse; mitengo yazipatso ndi yamikungudza yonse:

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Inu mapiri onse ndi zitunda zonse, inu mitengo yazipatso ndi mikungudza yonse!

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

inu mapiri ndi zitunda zonse, inu mitengo ya zipatso ndi mikungudza yonse,

Onani mutuwo



Masalimo 148:9
11 Mawu Ofanana  

Chipululu ndi mizinda yake ikweze mau ao, midzi imene Kedara akhalamo; okhala mu Sela aimbe, akuwe kuchokera pamwamba pa mapiri.


Imbani m'mwamba inu, pakuti Yehova wachichita icho; kuwani inu, mbali za pansi padziko; imbani mapiri inu; nkhalango iwe, ndi mitengo yonse m'menemo; chifukwa kuti Yehova wapulumutsa Yakobo, ndipo adzadzilemekezetsa yekha mwa Israele.


Imbani inu, m'mwamba, nukondwere iwe dziko lapansi, imbani inu mapiri, pakuti Yehova watonthoza mtima wa anthu ake, nadzachitira chifundo ovutidwa ake.


Mwenzi mutang'amba kumwamba ndi kutsikira pansi, kuti mapiri agwedezeke pamaso panu;