Ndipo kunatero kuti pakusendera munthu aliyense kudzamlambira, iye anatambasula dzanja lake, namgwira, nampsompsona.
Masalimo 10:10 - Buku Lopatulika Aunthama, nawerama, ndipo aumphawi agwa m'zala zake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Aunthama, nawerama, ndipo aumphawi agwa m'zala zake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amambwandira ndi kupsitiriza anthu osoŵa mwai, ndipo nyonga zake zimaŵagwetsa pansi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthuwo amawapondaponda ndipo amakomoka; amakhala pansi pa mphamvu zake. |
Ndipo kunatero kuti pakusendera munthu aliyense kudzamlambira, iye anatambasula dzanja lake, namgwira, nampsompsona.
Ndipo kudzali kuti yense wakusiyidwa wa m'banja lako adzabwera kwa iye nadzawerama ndi kupempha ndalama ndi chakudya, nadzati, Mundipatsetu ntchito ina ya wansembe, kuti ndikaone kakudya.