2 Samueli 15:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo kunatero kuti pakusendera munthu aliyense kudzamlambira, iye anatambasula dzanja lake, namgwira, nampsompsona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo kunatero kuti pakusendera munthu aliyense kudzamlambira, iye anatambasula dzanja lake, namgwira, nampsompsona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Choncho nthaŵi zonse munthu ankati akasendera pafupi kudzalambira Abisalomuyo, iye ankatambalitsa mkono, ndipo ankamgwira munthuyo namumpsompsona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndipo nthawi zonse amati munthu akasendera pafupi ndi kumugwandira, Abisalomu amatambalitsa dzanja lake, kumuyimiritsa munthuyo ndi kupsompsona. Onani mutuwo |