Masalimo 10:11 - Buku Lopatulika11 Anena m'mtima mwake, Mulungu waiwala; wabisa nkhope yake; sapenya nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Anena m'mtima mwake, Mulungu waiwala; wabisa nkhope yake; sapenya nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mumtima mwake amaganiza kuti, “Mulungu sasamalako, waphimba maso ake, sadzaziwona zimenezi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iye amati mu mtima mwake, “Mulungu wayiwala, wabisa nkhope yake ndipo sakuonanso.” Onani mutuwo |