Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 10:10 - Buku Lopatulika

10 Aunthama, nawerama, ndipo aumphawi agwa m'zala zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Aunthama, nawerama, ndipo aumphawi agwa m'zala zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Amambwandira ndi kupsitiriza anthu osoŵa mwai, ndipo nyonga zake zimaŵagwetsa pansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Anthuwo amawapondaponda ndipo amakomoka; amakhala pansi pa mphamvu zake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 10:10
4 Mawu Ofanana  

Ndipo kunatero kuti pakusendera munthu aliyense kudzamlambira, iye anatambasula dzanja lake, namgwira, nampsompsona.


Ndipo kudzali kuti yense wakusiyidwa wa m'banja lako adzabwera kwa iye nadzawerama ndi kupempha ndalama ndi chakudya, nadzati, Mundipatsetu ntchito ina ya wansembe, kuti ndikaone kakudya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa