Luka 4:11 - Buku Lopatulika Ndipo, Pa manja ao adzakunyamula iwe, kuti ungagunde konse phazi lako pamwala. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo, Pa manja ao adzakunyamula iwe, kuti ungagunde konse phazi lako pamwala. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “ ‘Iwo adzakunyamulani m'manja mwao, kuti mapazi anu angapweteke pa miyala.’ ” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo adzakunyamula ndi manja awo, kuti phazi lako lisagunde pa mwala.” |
nanena naye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, mudzigwetse nokha pansi: pakuti kwalembedwa, kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, ndipo pa manja ao adzakunyamula iwe, ungagunde konse phazi lako pamwala.