Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 91:12 - Buku Lopatulika

12 Adzakunyamula pa manja ao, ungagunde phazi lako pamwala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Adzakunyamula pa manja ao, ungagunde phazi lako pamwala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Adzakunyamula m'manja mwao, kuwopa kuti phazi lako lingapweteke ndi mwala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 ndipo adzakunyamula ndi manja awo, kuti phazi lako lisagunde pa mwala.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 91:12
7 Mawu Ofanana  

Pakuti udzakhala ndi pangano ndi miyala yakuthengo; ndi nyama zakuthengo zidzakhala nawe mumtendere.


Angakhale akagwa, satayikiratu, pakuti Yehova agwira dzanja lake.


Pompo udzayenda m'njira yako osaopa, osaphunthwa phazi lako.


Mverani Ine, banja la Yakobo, ndi otsala onse a banja la Israele, amene ndakunyamulani kuyambira m'mimba, ndi kukusenzani chibadwire;


M'mazunzo ao onse Iye anazunzidwa, ndipo mthenga wakuimirira pamaso pake anawapulumutsa; m'kukonda kwake ndi m'chisoni chake Iye anawaombola, nawabereka nawanyamula masiku onse akale.


nanena naye, Ngati muli Mwana wa Mulungu, mudzigwetse nokha pansi: pakuti kwalembedwa, kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, ndipo pa manja ao adzakunyamula iwe, ungagunde konse phazi lako pamwala.


Ndipo, Pa manja ao adzakunyamula iwe, kuti ungagunde konse phazi lako pamwala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa