Luka 4:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iye, Kwanenedwa, Usamuyese Ambuye Mulungu wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iye, Kwanenedwa, Usamuyese Ambuye Mulungu wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma Yesu adati, “Malembo akuti, ‘Usaŵayese Ambuye, Mulungu wako.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Yesu anayankha kuti, “Mawu akuti, ‘Musamuyese Yehova Mulungu wanu.’ ” Onani mutuwo |