Luka 4:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo mdierekezi, m'mene adamaliza mayesero onse, analekana naye kufikira nthawi ina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo mdierekezi, m'mene adamaliza mayesero onse, analekana naye kufikira nthawi ina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono Satana atatha kumuyesa mwa zonsezi, adalekana naye, kudikira nthaŵi ina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mdierekezi atamaliza mayesero awa onse, anamusiya Iye kufikira atapeza mpata wina. Onani mutuwo |