Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 4:14 - Buku Lopatulika

14 Ndipo Yesu anabwera ndi mphamvu ya Mzimu ku Galileya; ndipo mbiri yake ya Iye inabuka ku dziko lonse loyandikira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndipo Yesu anabwera ndi mphamvu ya Mzimu ku Galileya; ndipo mbiri yake ya Iye inabuka ku dziko lonse loyandikira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Yesu adabwereranso ku Galileya ndi mphamvu za Mzimu Woyera. Mbiri yake idawanda kuzungulira dziko lonselo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Yesu anabwerera ku Galileya mu mphamvu ya Mzimu Woyera, ndipo mbiri yake inafalikira ku madera onse a ku midzi.

Onani mutuwo Koperani




Luka 4:14
10 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene Yesu anamva kuti anampereka Yohane, anamuka kulowa ku Galileya;


Ndipo mbiri yake imene inabuka m'dziko lonse limenelo.


Koma iwo anatulukamo, nabukitsa mbiri yake m'dziko lonselo.


Ndipo ataperekedwa Yohane, Yesu anadza ku Galileya, nalalikira Uthenga Wabwino wa Mulungu,


Ndipo mbiri yake inabuka pompaja kudziko lonse la Galileya lozungulirapo.


Ndipo mdierekezi, m'mene adamaliza mayesero onse, analekana naye kufikira nthawi ina.


Ndipo mbiri yake ya Iye inafalikira kumalo onse a dziko loyandikira.


Koma atapita masiku awiriwo anachoka komweko kunka ku Galileya.


mauwo muwadziwa inu, adadzawo ku Yudeya lonse, akuyamba ku Galileya, ndi ubatizo umene Yohane anaulalikira;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa