Luka 4:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Iye anaphunzitsa m'masunagoge mwao, nalemekezedwa ndi anthu onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Iye anaphunzitsa m'masunagoge mwao, nalemekezedwa ndi anthu onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ankaphunzitsa m'nyumba zao zamapemphero, ndipo anthu onse ankamutamanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Iye ankaphunzitsa mʼmasunagoge awo, ndipo aliyense ankamulemekeza. Onani mutuwo |