Luka 4:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo, Pa manja ao adzakunyamula iwe, kuti ungagunde konse phazi lako pamwala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo, Pa manja ao adzakunyamula iwe, kuti ungagunde konse phazi lako pamwala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “ ‘Iwo adzakunyamulani m'manja mwao, kuti mapazi anu angapweteke pa miyala.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 ndipo adzakunyamula ndi manja awo, kuti phazi lako lisagunde pa mwala.” Onani mutuwo |