Luka 4:10 - Buku Lopatulika10 pakuti kwalembedwa kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, kuti akutchinjirize. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 pakuti kwalembedwa kuti, Adzalamula angelo ake za iwe, kuti akutchinjirize. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Paja Malembo akuti, “ ‘Mulungu adzalamula angelo ake kuti akusamaleni.’ Ndiponso, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pakuti kwalembedwa, “Adzalamulira angelo ake za iwe kuti akutchinjirize mosamala; Onani mutuwo |