Genesis 42:12 - Buku Lopatulika Ndipo iye anati kwa iwo, Iai, koma mwadzera kuti muone usiwa wa dziko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iye anati kwa iwo, Iai, koma mwadzera kuti muone usiwa wa dziko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yosefe adati, “Iyai. Inu mwabwera kudzazonda dziko lathu kuti muwone ngati ndi lofooka.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anawawuza kuti, “Ayi! Inu mwabwera kudzaona pamene palibe chitetezo mʼdziko muno.” |
Nati iwo, Akapolo anu ndife abale khumi, ana aamuna a munthu mmodzi m'dziko la Kanani; ndipo, taonani, wamng'ono ali ndi atate wathu lero; ndipo palibe mmodzi.
Mudzayesedwa ndi ichi, pali moyo wa Farao, simudzatuluka muno, koma akadze kuno mphwanu ndiko.
Mumdziwa Abinere mwana wa Nere kuti anadza kuti akunyengeni, ndi kuti adziwe kutuluka kwanu ndi kulowa kwanu, ndi kuti adziwe zonse mulikuchita inu.