Genesis 42:11 - Buku Lopatulika11 Tonse tili ana aamuna a munthu mmodzi; tili oona, akapolo anu, sitili ozonda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Tonse tili ana amuna a munthu mmodzi; tili oona, akapolo anu, sitili ozonda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tonsefe tili pachibale. Sindife azondi, mbuyathu, koma ndife anthu okhulupirika ndithu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tonse ndife ana a munthu mmodzi. Ndife antchito anu okhulupirika osati akazitape.” Onani mutuwo |