Genesis 42:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo iye anati kwa iwo, Iai, koma mwadzera kuti muone usiwa wa dziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo iye anati kwa iwo, Iai, koma mwadzera kuti muone usiwa wa dziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Yosefe adati, “Iyai. Inu mwabwera kudzazonda dziko lathu kuti muwone ngati ndi lofooka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iye anawawuza kuti, “Ayi! Inu mwabwera kudzaona pamene palibe chitetezo mʼdziko muno.” Onani mutuwo |