Genesis 10:17 - Buku Lopatulika ndi Ahivi, ndi Aariki, ndi Asini; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Ahivi, ndi Aariki, ndi Asini; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ahivi, Aariki, Asini, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ahivi, Aariki, Asini, |
ndi Aaravadi, ndi Aazemari, ndi Ahamati; pambuyo pake pamenepo ndipo mabanja a Akanani anafalikira.
Pamene anamuona iye Sekemu, mwana wake wamwamuna wa Hamori Muhivi, kalonga wa dzikolo, anamtenga nagona ndi iye, namuipitsa.
Ndipo anthu onse otsala mwa Ahiti, ndi Aamori, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi, osati Aisraele,
Ndipo amuna a Israele anati kwa Ahivi, Kapena mulimkukhala pakati pa ife, ndipo tipanganenji ndi inu?