Genesis 10:18 - Buku Lopatulika18 ndi Aaravadi, ndi Aazemari, ndi Ahamati; pambuyo pake pamenepo ndipo mabanja a Akanani anafalikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndi Aaravadi, ndi Aazemari, ndi Ahamati; pambuyo pake pamenepo ndipo mabanja a Akanani anafalikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Aaravadi, Azemari ndi Ahamati. Pambuyo pake mafuko a Akananiwo adabalalika ponseponse, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Aaravadi, Azemari ndi Ahamati. Pambuyo pake, mafuko a Akanaani anafalikira ponseponse, Onani mutuwo |