Eksodo 8:2 - Buku Lopatulika Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ukakana kuŵalola, dziko lako lonse ndidzalilanga polidzaza ndi achule. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ngati simulola kuti apite Ine ndidzalanga dziko lonse la Igupto polidzaza ndi achule. |
Ndipo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, nunene naye, Atero Yehova, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire.
ndipo m'mtsinjemo mudzachuluka achule, amene adzakwera nadzalowa m'nyumba mwako, ndi m'chipinda chogona iwe, ndi pakama pako, ndi m'nyumba ya anyamata ako, ndi pa anthu ako, m'michembo yanu yootcheramo, ndi m'mbale zanu zoumbiramo.