Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:45 - Buku Lopatulika

45 Anawatumizira pakati pao mitambo ya ntchentche zakuwatha; ndi achule akuwaononga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

45 Anawatumizira pakati pao mitambo ya ntchentche zakuwatha; ndi achule akuwaononga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

45 Adaŵatumira nthenje za ntchentche zimene zidaŵazunza, ndiponso achule amene adasakaza dziko lao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

45 Iye anawatumizira magulu a ntchentche zimene zinawawononga, ndiponso achule amene anawasakaza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:45
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anachita chomwecho; pakuti Aroni anasamula dzanja lake ndi ndodo yake, napanda fumbi lapansi, ndipo panali nsabwe pa anthu ndi pa zoweta; fumbi lonse lapansi linasanduka nsabwe m'dziko lonse la Ejipito.


Ndipo Yehova anati kwa Mose Uuke ulawire mamawa, nuime pamaso pa Farao; taona, atuluka kunka kumadzi; nunene naye, Atero Yehova, Lola anthu anga amuke, anditumikire.


Ndipo wachiwiri anatsanulira mbale yake m'nyanja; ndipo kunakhala mwazi ngati wa munthu wakufa; ndipo zamoyo zonse za m'nyanja zidafa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa