Eksodo 8:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo ngati simulola kuti apite Ine ndidzalanga dziko lonse la Igupto polidzaza ndi achule. Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ukakana kuŵalola, dziko lako lonse ndidzalilanga polidzaza ndi achule. Onani mutuwo |