Eksodo 8:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo ukakana kuwalola amuke, taona, Ine ndidzapanda dziko lako lonse ndi achule; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ukakana kuŵalola, dziko lako lonse ndidzalilanga polidzaza ndi achule. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo ngati simulola kuti apite Ine ndidzalanga dziko lonse la Igupto polidzaza ndi achule. Onani mutuwo |