Eksodo 6:22 - Buku Lopatulika Ndi ana aamuna a Uziyele ndiwo: Misaele, ndi Elizafani, ndi Sitiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ana amuna a Uziyele ndiwo: Misaele, ndi Elizafani, ndi Sitiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Uziyele naŵa: Misaele, Elizafani ndi Sitiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a Uzieli anali Misaeli, Elizafani ndi Sitiri. |
Potsatizana naye Baruki mwana wa Zabai anafulumira kukonza gawo lina kuyambira popindirira mpaka kukhomo la nyumba ya Eliyasibu mkulu wa ansembe.
Ndipo Mose anaitana Misaele ndi Elizafani, ana a Uziyele, mbale wa atate wa Aroni, nanena nao, Senderani pafupi, nyamulani abale anu muwachotse pakhomo pa malo opatulika kunka nao kunja kwa chigono.
Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo ao ya mabanja a Akohati ndiye Elizafani mwana wa Uziyele.