Eksodo 6:21 - Buku Lopatulika Ndi ana aamuna a Izihara ndiwo: Kora ndi Nefegi, ndi Zikiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ana amuna a Izihara ndiwo: Kora ndi Nefegi, ndi Zikiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Izihara naŵa: Kora, Nefegi ndi Zikiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a Izihari anali Kora, Nefegi ndi Zikiri. |
ndi wotsatana naye Amasiya mwana wa Zikiri, wodzipereka kwa Yehova mwaufulu, ndi pamodzi ndi iye ngwazi zamphamvu zikwi mazana awiri;
Ndipo ana aamuna a Kora ndiwo: Asiri ndi Elikana, ndi Abiyasafu; amenewo ndiwo mabanja a Akora.
Koma Kora, mwana wa Izihara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, anatenga Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, ndi Oni mwana wa Peleti, ana a Rubeni;
ndi dziko linayasama pakamwa pake ndi kuwameza, iwo ndi mabanja ao, ndi amuna ao onse akutsata Kora, ndi akatundu ao onse.