Eksodo 6:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo ana aamuna a Kora ndiwo: Asiri ndi Elikana, ndi Abiyasafu; amenewo ndiwo mabanja a Akora. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo ana amuna a Kora ndiwo: Asiri ndi Elikana, ndi Abiyasafu; amenewo ndiwo mabanja a Akora. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ana a Kora naŵa: Asiri, Elikana ndi Abiyasafu. Ameneŵa ndiwo mabanja a Kora. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ana a Kora anali Asiri, Elikana ndi Abiasafu. Awa ndiwo mafuko a Kora. Onani mutuwo |