Eksodo 6:22 - Buku Lopatulika22 Ndi ana aamuna a Uziyele ndiwo: Misaele, ndi Elizafani, ndi Sitiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndi ana amuna a Uziyele ndiwo: Misaele, ndi Elizafani, ndi Sitiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ana a Uziyele naŵa: Misaele, Elizafani ndi Sitiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ana a Uzieli anali Misaeli, Elizafani ndi Sitiri. Onani mutuwo |