Eksodo 6:19 - Buku Lopatulika Ndipo ana aamuna a Merari ndiwo: Mali ndi Musi. Amenewo ndiwo mabanja a Levi mwa kubadwa kwao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ana amuna a Merari ndiwo: Mali ndi Musi. Amenewo ndiwo mabanja a Levi mwa kubadwa kwao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Merari naŵa: Mali ndi Musi. Ameneŵa ndiwo mabanja a Levi pamodzi ndi zidzukulu zao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a Merari anali Mali ndi Musi. Awa anali mafuko a Levi monga mwa mibado yawo. |
Ana a Merari: Mali ndi Musi. Ndi mabanja a Alevi monga mwa nyumba za makolo ao ndi awa.
Ndi ana a Merari monga mwa mabanja ao: Mali ndi Musi. Awa ndi mabanja a Alevi monga mwa nyumba za makolo ao.
Ana a Merari, monga mwa mabanja ao, analandira motapa pa fuko la Rubeni, ndi pa fuko la Gadi, ndi pa fuko la Zebuloni mizinda khumi ndi iwiri.