Eksodo 6:17 - Buku Lopatulika Ana aamuna a Geresoni ndiwo: Libini ndi Simei, mwa mabanja ao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana amuna a Geresoni ndiwo: Libini ndi Simei, mwa mabanja ao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana a Geresoni naŵa: Libini ndi Simeyi pamodzi ndi mabanja ao. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a Geresoni, mwa mafuko awo, anali Libini ndi Simei. |
Ndipo ana a Geresoni analandira molota maere motapa pa mabanja a fuko la Isakara, ndi pa fuko la Asere, ndi pa fuko la Nafutali, ndi pa hafu la fuko la Manase mu Basani, mizinda khumi ndi itatu.