ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
Eksodo 38:6 - Buku Lopatulika Napanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi mkuwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Napanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi mkuwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adasema mphiko zonyamulira za mtengo wa kasiya, nazikuta ndi mkuŵa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anapanga nsichi zamtengo wa mkesha ndipo anazikuta ndi mkuwa. |
ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonyika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
Ndipo anapisa mphikozo mu mphetezo pa mbali za guwa la nsembe, kulinyamulira nazo; analipanga ndi matabwa, lagweregwere.
Potero ndinapanga likasa la mtengo wakasiya, ndinasemanso magome awiri amiyala onga oyamba aja, ndi kukwera m'phirimo, magome awiri ali m'manja mwanga.