Eksodo 38:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anayengera mathungo anai a sefa wamkuwayo mphete zinai, zikhale zopisamo mphiko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anayengera mathungo anai a sefa wamkuwayo mphete zinai, zikhale zopisamo mphiko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Adapanga mphete zinai ndipo adazilumikiza ku ngodya zinai za sefa ija, kuti apisemo mphiko zonyamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anapanga mphete zamkuwa zinayi ndipo anazilumikiza ku ngodya zinayi za sefa ija kuti zigwire nsichi zonyamulira. Onani mutuwo |