Eksodo 38:6 - Buku Lopatulika6 Napanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi mkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Napanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi mkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adasema mphiko zonyamulira za mtengo wa kasiya, nazikuta ndi mkuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Anapanga nsichi zamtengo wa mkesha ndipo anazikuta ndi mkuwa. Onani mutuwo |