Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 38:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Anapanga mphete zamkuwa zinayi ndipo anazilumikiza ku ngodya zinayi za sefa ija kuti zigwire nsichi zonyamulira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Ndipo anayengera mathungo anai a sefa wamkuwayo mphete zinai, zikhale zopisamo mphiko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo anayengera mathungo anai a sefa wamkuwayo mphete zinai, zikhale zopisamo mphiko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Adapanga mphete zinai ndipo adazilumikiza ku ngodya zinai za sefa ija, kuti apisemo mphiko zonyamulira.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 38:5
4 Mawu Ofanana  

Mphetezo uziyike kufupi ndi feremu kuti azikolowekamo nsichi zonyamulira tebuloyo.


Upange sefa yachitsulo chamkuwa ndipo mʼngodya zake zinayizo upangiremo mphete zamkuwa.


Anapanga sefa yachitsulo chamkuwa ya guwa lansembelo kuti ikhale mmunsi mwa khoma la guwa lansembelo, kuchokera pansi mpaka pakati pa khoma la guwalo.


Anapanga nsichi zamtengo wa mkesha ndipo anazikuta ndi mkuwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa