Eksodo 38:5 - Buku Lopatulika Ndipo anayengera mathungo anai a sefa wamkuwayo mphete zinai, zikhale zopisamo mphiko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anayengera mathungo anai a sefa wamkuwayo mphete zinai, zikhale zopisamo mphiko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adapanga mphete zinai ndipo adazilumikiza ku ngodya zinai za sefa ija, kuti apisemo mphiko zonyamulira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anapanga mphete zamkuwa zinayi ndipo anazilumikiza ku ngodya zinayi za sefa ija kuti zigwire nsichi zonyamulira. |
Ndipo ulipangire sefa, malukidwe ake ndi amkuwa; nupange pa malukidwewo ngodya zake zinai mphete zinai zamkuwa.
Ndipo anapangira guwa la nsembelo sefa, malukidwe ake nja mkuwa, pansi pa khoma lamkati lake wakulekeza pakati pake.