Eksodo 25:27 - Buku Lopatulika27 Mphetezo zikhale pafupi pa mitanda, zikhale zopisamo mphiko za kunyamulira nazo gome. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Mphetezo zikhale pafupi pa mitanda, zikhale zopisamo mphiko za kunyamulira nazo gome. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Mphete zopisamo mphiko zonyamulira tebulolo ziikidwe pafupi ndi fulemu lija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mphetezo uziyike kufupi ndi feremu kuti azikolowekamo nsichi zonyamulira tebuloyo. Onani mutuwo |