Eksodo 25:26 - Buku Lopatulika26 Nulipangire mphete zinai zagolide, ndi kuika mphetezo pangodya zinai zokhala pa miyendo yake inai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Nulipangire mphete zinai zagolide, ndi kuika mphetezo pangodya zinai zokhala pa miyendo yake inai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Upange mphete zinai zagolide, ndipo uzilumikize ku ngodya zinai za ku miyendo yake inai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Upange mphete zinayi zagolide, ndipo uzilumikize ku ngodya zake zinayi, kumene kuli miyendo yake inayi. Onani mutuwo |