Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 25:25 - Buku Lopatulika

25 Nulipangire mitanda pozungulirapo yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira upangirepo mkombero wagolide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Nulipangire mitanda pozungulirapo yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira upangirepo mkombero wagolide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Upange fulemu lozungulira tebulo, muufupi mwake kuyesa chikhatho, ndipo upange mkombero wagolide wozungulira fulemulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Upange feremu yozungulira tebulo, mulifupi mwake ngati chikhatho cha dzanja, ndipo uyike mkombero wagolide kuzungulira feremuyo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 25:25
7 Mawu Ofanana  

Ndi kuchindikira kwake kunanga chikhato, ndi mlomo wake unasadamuka ngati mlomo wa chomwera, ngati duwa la kakombo; analowamo madzi a mitsuko yaikulu zikwi zitatu.


Ndipo ulikute ndi golide woona ndi kulipangira mkombero wagolide pozungulira pake.


Nulipangire mphete zinai zagolide, ndi kuika mphetezo pangodya zinai zokhala pa miyendo yake inai.


Ndipo ulikute ndi golide woona, pamwamba pake ndi mbali zake zozungulira, ndi nyanga zake; ulipangirenso mkombero wagolide pozungulira.


Analipangiranso mitanda pozungulirapo, yoyesa chikhato m'kupingasa kwake, ndi pamitanda pake pozungulira anapangirapo mkombero wagolide.


ndipo analikuta ndi golide woona m'kati ndi kunja, nalipangira mkombero wa golide pozungulira pake.


Ndipo miyeso ya guwa la nsembe, kuyesa mikono ndi iyi: (mkonowo ndiwo mkono ndi chikhato), tsinde lake likhale mkono, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi, ndi mkuzi wake m'mphepete mwake pozungulira pake kuyesa zala; ili ndi tsinde la guwali.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa