Eksodo 25:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo ulikute ndi golide woona ndi kulipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo ulikute ndi golide woona ndi kulipangira mkombero wagolide pozungulira pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono ulikute ndi golide wabwino kwambiri ndipo pozungulira pake ponse upange mkombero wagolide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Tebulolo ulikute ndi golide wabwino kwambiri ndipo upange mkombero wagolide mʼmbali mwake. Onani mutuwo |