Eksodo 25:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo uzipanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo uzipanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Upange tebulo la matabwa a mtengo wa kasiya, kutalika kwake masentimita 91, muufupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 “Upange tebulo la matabwa amtengo wa mkesha, mulitali mwake masentimita 91, mulifupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69. Onani mutuwo |