Eksodo 25:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo pomwepo ndidzakomana ndi iwe, ndi kulankhula ndi iwe, ndili pamwamba pa chotetezerapo, pakati pa akerubi awiriwo okhala pa likasa la mboni, zonse zimene ndidzakuuza za ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo pomwepo ndidzakomana ndi iwe, ndi kulankhula ndi iwe, ndili pamwamba pa chotetezerapo, pakati pa akerubi awiriwo okhala pa likasa la mboni, zonse zimene ndidzakuuza za ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Ndizidzakumana nawe kumeneko, ndipo kuchokera pamwamba pa chivundikirocho, pakati pa akerubi ali pamwamba pa bokosiwo, ndidzakuuza malamulo okhudza anthu anga Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndizidzakumana nawe pamenepo, pamwamba pa chivundikiro cha bokosilo, pakati pa Akerubi awiriwo, ndikumadzakupatsa malamulo onse okhudzana ndi Aisraeli. Onani mutuwo |