Eksodo 25:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo uziika chotetezerapo pamwamba pa likasa, ndi kuikamo mboni ndidzakupatsayo m'likasamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo uziika chotetezerapo pamwamba pa likasa, ndi kuikamo mboni ndidzakupatsayo m'likasamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Chivundikiro cha bokosicho udzachiike pamwamba pa bokosilo, ndipo m'bokosimo udzaikemo miyala iŵiri ija ya Malamulo imene ndidzakupatse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Uyike chivundikirocho pamwamba pa bokosi ndipo mʼbokosilo uyikemo miyala ya malamulo, imene ndidzakupatse. Onani mutuwo |