Eksodo 31:8 - Buku Lopatulika ndi gomelo ndi zipangizo zake, ndi choikaponyali choona ndi zipangizo zake, ndi guwa la nsembe lofukizapo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi gomelo ndi zipangizo zake, ndi choikapo nyali choona ndi zipangizo zake, ndi guwa la nsembe lofukizapo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa tebulo ndi zipangizo zake, choikaponyale cha golide wabwino kwambiri, pamodzi ndi zipangizo zake, guwa lofukizirapo lubani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero tebulo ndi zida zake, choyikapo nyale cha golide wabwino kwambiri ndi ziwiya zake zonse, guwa lofukizirapo lubani, |
Kapena sayatsa nyali, ndi kuivundikira m'mbiya, koma aiika iyo pa choikapo chake; ndipo iunikira onse ali m'nyumbamo.