Eksodo 31:9 - Buku Lopatulika9 ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate ndi tsinde lake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndi guwa la nsembe yopsereza ndi zipangizo zake zonse, ndi mkhate ndi tsinde lake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 guwa la zopereka zopsereza, pamodzi ndi zipangizo zake, beseni losambira ndi phaka lake, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 guwa lansembe yopsereza ndi ziwiya zake zonse, beseni ndi nsichi yake, Onani mutuwo |