Eksodo 31:10 - Buku Lopatulika10 ndi zovala zotumikira nazo, ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, ndi zovala za ana ake, zakuchita nazo ntchito ya nsembe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndi zovala zotumikira nazo, ndi zovala zopatulika za Aroni wansembe, ndi zovala za ana ake, zakuchita nazo ntchito ya nsembe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 zovala zopatulika za wansembe Aroni ndi za ana ake, zomavala pa nthaŵi imene akutumikira, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 ndiponso zovala zonse zolukidwa, zovala zopatulika za Aaroni wansembe pamodzi ndi za ana ake, zovala pamene akutumikira monga ansembe, Onani mutuwo |