Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 31:11 - Buku Lopatulika

11 ndi mafuta odzoza, ndi chofukiza cha zonunkhira zokoma za malo opatulika; azichita monga mwa zonse ndakuuza iwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 ndi mafuta odzoza, ndi chofukiza cha zonunkhira zokoma za malo opatulika; azichita monga mwa zonse ndakuuza iwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 mafuta odzozera ndiponso lubani wa fungo lokoma, zonsezo zokhalira malo oyera. Adzapange zinthu zonsezi monga ndakulamulira iwe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 ndiponso mafuta odzozera ndi lubani wonunkhira wa ku malo opatulika. Iwo azipanga monga momwe Ine ndinakulamulira.”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 31:11
5 Mawu Ofanana  

Ndipo uyang'anire uzipanga monga mwachifaniziro chao, chimene anakuonetsa m'phirimo.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,


Pamenepo anachita Bezalele ndi Oholiyabu, ndi anthu aluso, amene Yehova adaika luso ndi nzeru m'mtima mwao adziwe machitidwe ake a ntchito yonse ya utumiki wake wa malo opatulika, monga mwa zonse adauza Yehova.


Anapanganso mafuta opatulika akudzoza nao, ndi chofukiza choona cha fungo lokoma, mwa machitidwe a wosakaniza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa