Eksodo 31:8 - Buku Lopatulika8 ndi gomelo ndi zipangizo zake, ndi choikaponyali choona ndi zipangizo zake, ndi guwa la nsembe lofukizapo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndi gomelo ndi zipangizo zake, ndi choikapo nyali choona ndi zipangizo zake, ndi guwa la nsembe lofukizapo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 tebulo ndi zipangizo zake, choikaponyale cha golide wabwino kwambiri, pamodzi ndi zipangizo zake, guwa lofukizirapo lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 tebulo ndi zida zake, choyikapo nyale cha golide wabwino kwambiri ndi ziwiya zake zonse, guwa lofukizirapo lubani, Onani mutuwo |