Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 31:7 - Buku Lopatulika

7 chihema chokomanako, likasa la mboni, ndi chotetezerapo chili pamwamba pake, ndi zipangizo zonse za chihemacho;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 chihema chokomanako, likasa la mboni, ndi chotetezerapo chili pamwamba pake, ndi zipangizo zonse za chihemacho;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Apange chihema chamsonkhano Ine ndi anthu anga, bokosi lachipangano, chivundikiro cha bokosi, pamodzi ndi zipangizo za chihema,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Kupanga tenti ya msonkhano, bokosi laumboni pamodzi ndi chophimbira chake, ndiponso zonse za mu tenti,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 31:7
9 Mawu Ofanana  

Ndipo onse a mtima waluso mwa iwo akuchita ntchitoyi anapanga chihema ndi nsalu zophimba khumi; anaziomba ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi akerubi, ntchito ya mmisiri.


Ndipo Bezalele anapanga likasa la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;


Ndipo anapanga chotetezerapo cha golide woona; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu.


Potero anatsiriza ntchito yonse ya Kachisi wa chihema chokomanako; ndipo ana a Israele adachita monga mwa zonse Yehova adamuuza Mose, anachita momwemo.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,


Ndipo ukaikemo likasa la mboni, nutchinge likasalo ndi nsalu yotchingayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa