Eksodo 31:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Ine, taona, ndampatsa Oholiyabu, mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani, akhale naye; ndipo ndaika luso m'mitima ya onse a mtima waluso, kuti apange zonse ndakuuza iwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Ine, taona, ndampatsa Oholiyabu, mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani, akhale naye; ndipo ndaika luso m'mitima ya onse a mtima waluso, kuti apange zonse ndakuuza iwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndasankhanso Aholiyabu mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani. Ndipo anthu ena onse aluso ndaŵapatsa nzeru zambiri zoti athe kupanga chinthu chilichonse chimene ndingakulamule kuti iwoŵa apange. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndasankhanso Oholiabu mwana wa Ahisamaki wa fuko la Dani. Ndiponso ndapereka nzeru kwa anthu aluso motero adzagwira ntchito zonse zimene ndakulamulira kuti zichitike monga izi: Onani mutuwo |